2 Mbiri 6:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Komanso mlendo amene si mmodzi wa anthu anu Aisiraeli, amene wabwera kuchokera kudziko lakutali chifukwa cha dzina* lanu lalikulu,+ dzanja lanu lamphamvu ndiponso mkono wanu wokonzeka kuthandiza,* ndipo wabwera nʼkupemphera atayangʼana nyumbayi,+
32 Komanso mlendo amene si mmodzi wa anthu anu Aisiraeli, amene wabwera kuchokera kudziko lakutali chifukwa cha dzina* lanu lalikulu,+ dzanja lanu lamphamvu ndiponso mkono wanu wokonzeka kuthandiza,* ndipo wabwera nʼkupemphera atayangʼana nyumbayi,+