2 Mbiri 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 inenso ndidzakhazikitsa mpando wako wachifumu,+ ngati mmene ndinapanganirana ndi bambo ako Davide+ kuti, ‘Munthu wa mʼbanja lako sadzachoka pampando wachifumu wa Isiraeli.’+
18 inenso ndidzakhazikitsa mpando wako wachifumu,+ ngati mmene ndinapanganirana ndi bambo ako Davide+ kuti, ‘Munthu wa mʼbanja lako sadzachoka pampando wachifumu wa Isiraeli.’+