2 Mbiri 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo adzati, ‘Nʼchifukwa chakuti anasiya Yehova+ Mulungu wa makolo awo amene anawatulutsa mʼdziko la Iguputo+ ndipo anatenga milungu ina nʼkumaigwadira ndi kuitumikira.+ Nʼchifukwa chake iye anawabweretsera tsoka lonseli.’”+
22 Ndipo adzati, ‘Nʼchifukwa chakuti anasiya Yehova+ Mulungu wa makolo awo amene anawatulutsa mʼdziko la Iguputo+ ndipo anatenga milungu ina nʼkumaigwadira ndi kuitumikira.+ Nʼchifukwa chake iye anawabweretsera tsoka lonseli.’”+