2 Mbiri 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako Solomo anapereka nsembe zopsereza+ kwa Yehova paguwa lansembe+ la Yehova limene iye anamanga patsogolo pa khonde.+
12 Kenako Solomo anapereka nsembe zopsereza+ kwa Yehova paguwa lansembe+ la Yehova limene iye anamanga patsogolo pa khonde.+