2 Mbiri 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho ntchito yonse ya Solomo inkayenda bwino, kuyambira tsiku limene anayala maziko a nyumba ya Yehova+ mpaka pamene inatha. Choncho nyumba ya Yehova inatha kumangidwa.+
16 Choncho ntchito yonse ya Solomo inkayenda bwino, kuyambira tsiku limene anayala maziko a nyumba ya Yehova+ mpaka pamene inatha. Choncho nyumba ya Yehova inatha kumangidwa.+