2 Mbiri 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Nayonso Mfumu Solomo inapatsa mfumukazi ya ku Sheba chilichonse chimene inkafuna komanso chimene inapempha. Inapatsa mfumukaziyo zoposa zimene inabweretsa. Kenako mfumukaziyo inanyamuka nʼkumapita kwawo limodzi ndi antchito ake.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:12 Nsanja ya Olonda,11/1/1999, tsa. 20
12 Nayonso Mfumu Solomo inapatsa mfumukazi ya ku Sheba chilichonse chimene inkafuna komanso chimene inapempha. Inapatsa mfumukaziyo zoposa zimene inabweretsa. Kenako mfumukaziyo inanyamuka nʼkumapita kwawo limodzi ndi antchito ake.+