2 Mbiri 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Makapu onse a Mfumu Solomo anali agolide, ndipo ziwiya zonse zamʼnyumba yotchedwa Nkhalango ya Lebanoni zinali zagolide yekhayekha. Panalibe chiwiya chasiliva chifukwa siliva sankaoneka ngati kanthu mʼmasiku a Solomo.+
20 Makapu onse a Mfumu Solomo anali agolide, ndipo ziwiya zonse zamʼnyumba yotchedwa Nkhalango ya Lebanoni zinali zagolide yekhayekha. Panalibe chiwiya chasiliva chifukwa siliva sankaoneka ngati kanthu mʼmasiku a Solomo.+