2 Mbiri 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Solomo anali ndi makola 4,000 a mahatchi ndi magaleta komanso mahatchi* okwana 12,000.+ Zonsezi ankazisunga mʼmizinda yosungiramo magaleta ndiponso pafupi ndi mfumuyo ku Yerusalemu.+
25 Solomo anali ndi makola 4,000 a mahatchi ndi magaleta komanso mahatchi* okwana 12,000.+ Zonsezi ankazisunga mʼmizinda yosungiramo magaleta ndiponso pafupi ndi mfumuyo ku Yerusalemu.+