2 Mbiri 9:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Anthu ankamubweretsera Solomo mahatchi kuchokera ku Iguputo+ ndi kumayiko ena onse.