2 Mbiri 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Rehobowamu atamva zimenezi anauza anthuwo kuti: “Mukabwerenso pakatha masiku atatu.” Choncho anthuwo anapitadi.+
5 Rehobowamu atamva zimenezi anauza anthuwo kuti: “Mukabwerenso pakatha masiku atatu.” Choncho anthuwo anapitadi.+