-
2 Mbiri 10:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Bambo anga anakusenzetsani goli lolemera koma ineyo ndiwonjezera goli lanulo. Bambo anga ankakukwapulani ndi zikwapu koma ineyo ndizikukwapulani ndi zikoti zaminga.’”
-