2 Mbiri 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma Rehobowamu anapitiriza kulamulira Aisiraeli amene ankakhala mʼmizinda ya ku Yuda.+