-
2 Mbiri 11:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ansembe ndi Alevi amene anali mʼmadera onse mu Isiraeli anakhala kumbali ya Rehobowamu, ndipo anabwera kuchokera mʼmadera awo onse.
-