-
2 Mbiri 11:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Iwo analimbitsa ufumu wa Yuda ndiponso kuthandiza Rehobowamu mwana wa Solomo kwa zaka zitatu, popeza anthuwo anayenda mʼnjira ya Davide ndi ya Solomo kwa zaka zitatu.
-