2 Mbiri 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Rehobowamu ankakonda kwambiri Maaka mdzukulu wa Abisalomu kuposa akazi ake ena onse ndi akazi ake aangʼono.*+ Iye anakwatira akazi 18 ndipo anali ndi akazi aangʼono 60. Iye anabereka ana aamuna 28 ndi ana aakazi 60.
21 Rehobowamu ankakonda kwambiri Maaka mdzukulu wa Abisalomu kuposa akazi ake ena onse ndi akazi ake aangʼono.*+ Iye anakwatira akazi 18 ndipo anali ndi akazi aangʼono 60. Iye anabereka ana aamuna 28 ndi ana aakazi 60.