2 Mbiri 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komabe anachita mozindikira chifukwa anapititsa ana ake ena mʼmadera onse a ku Yuda ndi ku Benjamini komanso mʼmizinda yonse yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+ Anawapatsa zinthu zambiri nʼkuwapezeranso akazi ambirimbiri.
23 Komabe anachita mozindikira chifukwa anapititsa ana ake ena mʼmadera onse a ku Yuda ndi ku Benjamini komanso mʼmizinda yonse yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+ Anawapatsa zinthu zambiri nʼkuwapezeranso akazi ambirimbiri.