2 Mbiri 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Akalonga a Isiraeliwo ndi mfumuyo atamva zimenezi, anadzichepetsa+ nʼkunena kuti: “Yehova ndi wolungama.”
6 Akalonga a Isiraeliwo ndi mfumuyo atamva zimenezi, anadzichepetsa+ nʼkunena kuti: “Yehova ndi wolungama.”