2 Mbiri 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova ataona kuti anthuwo adzichepetsa, Yehovayo anauza Semaya kuti: “Anthuwa adzichepetsa, choncho sindiwawononga.+ Posachedwapa ndiwapulumutsa, ndipo Yerusalemu sindidzamusonyeza mkwiyo wanga kudzera mwa Sisaki.
7 Yehova ataona kuti anthuwo adzichepetsa, Yehovayo anauza Semaya kuti: “Anthuwa adzichepetsa, choncho sindiwawononga.+ Posachedwapa ndiwapulumutsa, ndipo Yerusalemu sindidzamusonyeza mkwiyo wanga kudzera mwa Sisaki.