-
2 Mbiri 12:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Nthawi iliyonse imene mfumuyo ikupita kunyumba ya Yehova, asilikaliwo ankanyamula zishangozo ndipo kenako ankazibwezera kuchipinda cha alonda.
-