2 Mbiri 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako Rehobowamu, mofanana ndi makolo ake, anamwalira nʼkuikidwa mʼmanda mu Mzinda wa Davide.+ Ndiyeno Abiya+ mwana wa Rehobowamu anayamba kulamulira mʼmalo mwake.
16 Kenako Rehobowamu, mofanana ndi makolo ake, anamwalira nʼkuikidwa mʼmanda mu Mzinda wa Davide.+ Ndiyeno Abiya+ mwana wa Rehobowamu anayamba kulamulira mʼmalo mwake.