-
2 Mbiri 13:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Koma Yerobowamu anatumiza asilikali kuti akawabisalire kumbuyo, choncho Yerobowamuyo ndi asilikali ena anakhala kutsogolo kwa Ayuda ndipo obisalawo anali kumbuyo kwa Ayudawo.
-