2 Mbiri 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Abiya ndi anthu ake anapha Aisiraeli ambirimbiri. Anapitiriza kupha Aisiraeliwo moti asilikali ophunzitsidwa bwino* okwana 500,000, anaphedwa.
17 Abiya ndi anthu ake anapha Aisiraeli ambirimbiri. Anapitiriza kupha Aisiraeliwo moti asilikali ophunzitsidwa bwino* okwana 500,000, anaphedwa.