2 Mbiri 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho pa nthawiyi Aisiraeli anachititsidwa manyazi, koma Ayuda anapambana chifukwa anadalira Yehova Mulungu wa makolo awo.+
18 Choncho pa nthawiyi Aisiraeli anachititsidwa manyazi, koma Ayuda anapambana chifukwa anadalira Yehova Mulungu wa makolo awo.+