2 Mbiri 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Abiya anapitiriza kuthamangitsa Yerobowamu ndipo anamulanda mizinda yake. Analanda Beteli+ ndi midzi yake yozungulira, Yesana ndi midzi yake yozungulira ndiponso Efuraini+ ndi midzi yake yozungulira.
19 Abiya anapitiriza kuthamangitsa Yerobowamu ndipo anamulanda mizinda yake. Analanda Beteli+ ndi midzi yake yozungulira, Yesana ndi midzi yake yozungulira ndiponso Efuraini+ ndi midzi yake yozungulira.