2 Mbiri 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye anabweretsa kunyumba ya Mulungu woona zinthu zimene bambo ake komanso iyeyo anaziyeretsa. Zinthuzo zinali siliva, golide ndi ziwiya zina zosiyanasiyana.+
18 Iye anabweretsa kunyumba ya Mulungu woona zinthu zimene bambo ake komanso iyeyo anaziyeretsa. Zinthuzo zinali siliva, golide ndi ziwiya zina zosiyanasiyana.+