2 Mbiri 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Asa, mofanana ndi makolo ake, anamwalira+ mʼchaka cha 41 cha ulamuliro wake.