2 Mbiri 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anawaitana pamodzi ndi Alevi awa: Semaya, Netaniya, Zebadiya, Asaheli, Semiramoti, Yehonatani, Adoniya, Tobiya ndi Tobi-adoniya, pamodzinso ndi Elisama ndi Yehoramu omwe anali ansembe.+
8 Anawaitana pamodzi ndi Alevi awa: Semaya, Netaniya, Zebadiya, Asaheli, Semiramoti, Yehonatani, Adoniya, Tobiya ndi Tobi-adoniya, pamodzinso ndi Elisama ndi Yehoramu omwe anali ansembe.+