2 Mbiri 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Asilikaliwa anawagawa mʼmagulu potsata nyumba za makolo awo: Adinala anali mmodzi wa atsogoleri a magulu a asilikali 1,000 a fuko la Yuda. Iye anali ndi asilikali amphamvu okwana 300,000.+
14 Asilikaliwa anawagawa mʼmagulu potsata nyumba za makolo awo: Adinala anali mmodzi wa atsogoleri a magulu a asilikali 1,000 a fuko la Yuda. Iye anali ndi asilikali amphamvu okwana 300,000.+