2 Mbiri 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amenewa ankatumikira mfumu, kuwonjezera pa anthu amene mfumuyo inawaika mʼmizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri mʼdziko lonse la Yuda.+
19 Amenewa ankatumikira mfumu, kuwonjezera pa anthu amene mfumuyo inawaika mʼmizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri mʼdziko lonse la Yuda.+