-
2 Mbiri 18:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ahabu mfumu ya Isiraeli anafunsa Yehosafati mfumu ya Yuda kuti: “Kodi tipita limodzi ku Ramoti-giliyadi?” Iye anamuyankha kuti: “Inu ndi ine ndife amodzi. Anthu anga ndi anthu anu ndi amodzi ndipo tikuthandizani pa nkhondoyi.”
-