2 Mbiri 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Yehosafati anauza mfumu ya Isiraeli kuti: “Choyamba, mufunsire kaye kwa Yehova.”+