2 Mbiri 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Aneneri ena onse ankaloseranso zofanana ndi zimenezi. Ankanena kuti: “Pitani ku Ramoti-giliyadi ndipo mukapambana.+ Yehova akapereka mzindawo kwa inu mfumu.”
11 Aneneri ena onse ankaloseranso zofanana ndi zimenezi. Ankanena kuti: “Pitani ku Ramoti-giliyadi ndipo mukapambana.+ Yehova akapereka mzindawo kwa inu mfumu.”