2 Mbiri 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno mfumu ya Isiraeli inauza Yehosafati kuti: “Paja ndinakuuzani kuti, ‘Sadzalosera zabwino za ine, koma zoipa.’”+
17 Ndiyeno mfumu ya Isiraeli inauza Yehosafati kuti: “Paja ndinakuuzani kuti, ‘Sadzalosera zabwino za ine, koma zoipa.’”+