-
2 Mbiri 18:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Iye anayankha kuti, ‘Ndipita kukakhala mzimu wabodza mʼkamwa mwa aneneri ake onse.’ Ndiyeno Mulungu anati, ‘Ukamʼpusitsadi ndipo zikakuyendera bwino. Pita ukachite zimenezo.’
-