2 Mbiri 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Zedekiya+ mwana wa Kenaana anapita pomwe panali Mikaya+ nʼkumumenya mbama+ ndipo ananena kuti: “Zingatheke bwanji kuti mzimu wa Yehova undidutse nʼkukalankhula ndi iwe?”+
23 Zedekiya+ mwana wa Kenaana anapita pomwe panali Mikaya+ nʼkumumenya mbama+ ndipo ananena kuti: “Zingatheke bwanji kuti mzimu wa Yehova undidutse nʼkukalankhula ndi iwe?”+