2 Mbiri 18:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mukawauze kuti, ‘Mfumu yanena kuti: “Mʼtsekereni munthu uyu.+ Muzimʼpatsa chakudya chochepa ndi madzi ochepa mpaka nditabwerako mwamtendere.”’”
26 Mukawauze kuti, ‘Mfumu yanena kuti: “Mʼtsekereni munthu uyu.+ Muzimʼpatsa chakudya chochepa ndi madzi ochepa mpaka nditabwerako mwamtendere.”’”