2 Mbiri 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Zitatero mfumu ya Isiraeli ndi Yehosafati mfumu ya Yuda ananyamuka kupita ku Ramoti-giliyadi.+