-
2 Mbiri 18:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Akuluakulu oyangʼanira asilikali okwera magaleta aja atangomuona Yehosafati, anaganiza kuti: “Mfumu ya Isiraeli ija ndi imeneyi.” Choncho anatembenuka kuti amenyane naye ndipo Yehosafati anayamba kukuwa kuti anthu amuthandize,+ ndipo Yehova anamuthandiza. Nthawi yomweyo Mulungu anawachititsa kuti amusiye.
-