-
2 Mbiri 20:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Kenako mzimu wa Yehova unafika pa Yahazieli yemwe anali pagulu la anthuwo. Iye anali mwana wa Zekariya, Zekariya anali mwana wa Benaya, Benaya anali mwana wa Yeyeli, Yeyeli anali mwana wa Mataniya, Mataniya anali Mlevi, mmodzi wa ana a Asafu.
-