2 Mbiri 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho Yahazieli anati: “Tamverani Ayuda nonsenu, anthu a ku Yerusalemu ndi inu Mfumu Yehosafati! Yehova akukuuzani kuti, ‘Musaope kapena kuchita mantha ndi gulu lalikululi chifukwa nkhondoyi si yanu, ndi ya Mulungu.+
15 Choncho Yahazieli anati: “Tamverani Ayuda nonsenu, anthu a ku Yerusalemu ndi inu Mfumu Yehosafati! Yehova akukuuzani kuti, ‘Musaope kapena kuchita mantha ndi gulu lalikululi chifukwa nkhondoyi si yanu, ndi ya Mulungu.+