2 Mbiri 20:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthuwo atayamba kuimba nyimbo zotamanda Mulungu mosangalala, Yehova anakonza zoti Aamoni, Amowabu ndi anthu akudera lamapiri la Seiri, omwe ankapita ku Yuda, aukiridwe mwadzidzidzi ndipo iwo anayamba kuphana okhaokha.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:22 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, ptsa. 20-21
22 Anthuwo atayamba kuimba nyimbo zotamanda Mulungu mosangalala, Yehova anakonza zoti Aamoni, Amowabu ndi anthu akudera lamapiri la Seiri, omwe ankapita ku Yuda, aukiridwe mwadzidzidzi ndipo iwo anayamba kuphana okhaokha.+