2 Mbiri 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ayuda atafika pansanja ya mlonda yamʼchipululu+ nʼkuyangʼana chigulu cha anthu chija, anangoona mitembo yokhayokha ili pansi+ popanda wopulumuka.
24 Ayuda atafika pansanja ya mlonda yamʼchipululu+ nʼkuyangʼana chigulu cha anthu chija, anangoona mitembo yokhayokha ili pansi+ popanda wopulumuka.