2 Mbiri 20:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Yehosafati anapitiriza kuyenda mʼnjira za Asa,+ bambo ake. Sanasiye kuyenda mʼnjirazo ndipo anachita zoyenera pamaso pa Yehova.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:32 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2017, tsa. 20
32 Yehosafati anapitiriza kuyenda mʼnjira za Asa,+ bambo ake. Sanasiye kuyenda mʼnjirazo ndipo anachita zoyenera pamaso pa Yehova.+