2 Mbiri 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho anamuika mʼmanda a mafumu mu Mzinda wa Davide,+ chifukwa anachita zinthu zabwino mu Isiraeli+ zokhudza Mulungu woona ndi nyumba ya Mulungu woonayo.
16 Choncho anamuika mʼmanda a mafumu mu Mzinda wa Davide,+ chifukwa anachita zinthu zabwino mu Isiraeli+ zokhudza Mulungu woona ndi nyumba ya Mulungu woonayo.