2 Mbiri 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inuyo mupite nokha kukamenya nkhondo ndipo limbani mtima. Kupanda kutero Mulungu woona angachititse kuti mugonje kwa adani anu, chifukwa Mulungu ali ndi mphamvu zomuthandiza+ munthu kapena zomʼchititsa kugonja.”
8 Inuyo mupite nokha kukamenya nkhondo ndipo limbani mtima. Kupanda kutero Mulungu woona angachititse kuti mugonje kwa adani anu, chifukwa Mulungu ali ndi mphamvu zomuthandiza+ munthu kapena zomʼchititsa kugonja.”