2 Mbiri 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Amaziya analimba mtima nʼkutsogolera asilikali ake kupita kuchigwa cha Mchere.+ Kumeneko anapha anthu okwana 10,000 a ku Seiri.+
11 Ndiyeno Amaziya analimba mtima nʼkutsogolera asilikali ake kupita kuchigwa cha Mchere.+ Kumeneko anapha anthu okwana 10,000 a ku Seiri.+