2 Mbiri 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma asilikali amene Amaziya anawabweza kuti asapite naye kunkhondo aja,+ anayamba kuukira mizinda ya Yuda kuyambira ku Samariya+ mpaka ku Beti-horoni,+ ndipo anapha anthu 3,000 amʼmizindayo nʼkutenga zinthu zambiri.
13 Koma asilikali amene Amaziya anawabweza kuti asapite naye kunkhondo aja,+ anayamba kuukira mizinda ya Yuda kuyambira ku Samariya+ mpaka ku Beti-horoni,+ ndipo anapha anthu 3,000 amʼmizindayo nʼkutenga zinthu zambiri.