2 Mbiri 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho Yehova anakwiyira kwambiri Amaziya ndipo anatumiza mneneri kukamʼfunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukutsatira milungu yomwe sinapulumutse anthu awo mʼmanja mwanu?”+
15 Choncho Yehova anakwiyira kwambiri Amaziya ndipo anatumiza mneneri kukamʼfunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukutsatira milungu yomwe sinapulumutse anthu awo mʼmanja mwanu?”+