2 Mbiri 25:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ukunena kuti, ‘Ine ndagonjetsa Edomu.’+ Choncho wayamba kukula mtima ndipo ukufuna kulemekezedwa. Khala mʼnyumba* mwako momwemo. Nʼchifukwa chiyani ukuputa tsoka chonsecho iwe ndi Ayudawo mugonja?”
19 Ukunena kuti, ‘Ine ndagonjetsa Edomu.’+ Choncho wayamba kukula mtima ndipo ukufuna kulemekezedwa. Khala mʼnyumba* mwako momwemo. Nʼchifukwa chiyani ukuputa tsoka chonsecho iwe ndi Ayudawo mugonja?”