2 Mbiri 25:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pankhondoyo, Ayuda anagonjetsedwa ndi Aisiraeli moti aliyense anathawira kunyumba* kwake.